2 Mafumu 17:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Aava anapanga Nibazi ndi Tarataka, pamene Asefaravaimu ankawotcha ana awo aamuna pamoto powapereka nsembe kwa Adarameleki ndi Anameleki, milungu ya Sefaravaimu.+
31 Aava anapanga Nibazi ndi Tarataka, pamene Asefaravaimu ankawotcha ana awo aamuna pamoto powapereka nsembe kwa Adarameleki ndi Anameleki, milungu ya Sefaravaimu.+