2 Mafumu 17:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Choncho ankaopa Yehova koma ankalambira milungu yawo, mogwirizana ndi chipembedzo cha mitundu imene anawatengako.+
33 Choncho ankaopa Yehova koma ankalambira milungu yawo, mogwirizana ndi chipembedzo cha mitundu imene anawatengako.+