2 Mafumu 17:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Mpaka lero akutsatirabe zipembedzo zawo zakale. Palibe amene akulambira* Yehova ndipo palibe amene akutsatira malamulo ake, ziweruzo zake ndiponso Chilamulo chimene Yehova anapatsa ana a Yakobo yemwe Mulungu anamusintha dzina nʼkukhala Isiraeli.+
34 Mpaka lero akutsatirabe zipembedzo zawo zakale. Palibe amene akulambira* Yehova ndipo palibe amene akutsatira malamulo ake, ziweruzo zake ndiponso Chilamulo chimene Yehova anapatsa ana a Yakobo yemwe Mulungu anamusintha dzina nʼkukhala Isiraeli.+