2 Mafumu 17:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Pamene Yehova anachita nawo pangano,+ anawalamula kuti: “Musamaope milungu ina. Musamaigwadire, kapena kuitumikira kapena kupereka nsembe kwa milunguyo.+
35 Pamene Yehova anachita nawo pangano,+ anawalamula kuti: “Musamaope milungu ina. Musamaigwadire, kapena kuitumikira kapena kupereka nsembe kwa milunguyo.+