2 Mafumu 18:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Hezekiya anakhala mfumu ali ndi zaka 25 ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 29. Mayi ake dzina lawo linali Abi* mwana wa Zekariya.+
2 Hezekiya anakhala mfumu ali ndi zaka 25 ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 29. Mayi ake dzina lawo linali Abi* mwana wa Zekariya.+