2 Mafumu 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye ankadalira Yehova+ Mulungu wa Isiraeli. Pa mafumu onse a Yuda amene anakhalapo iye asanakhale mfumu, ngakhalenso amene anakhalapo iye atafa, palibe amene anafanana naye.
5 Iye ankadalira Yehova+ Mulungu wa Isiraeli. Pa mafumu onse a Yuda amene anakhalapo iye asanakhale mfumu, ngakhalenso amene anakhalapo iye atafa, palibe amene anafanana naye.