2 Mafumu 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova anali naye ndipo kulikonse kumene ankapita ankachita zinthu mwanzeru. Anagalukira mfumu ya Asuri ndipo ankakana kuitumikira.+
7 Yehova anali naye ndipo kulikonse kumene ankapita ankachita zinthu mwanzeru. Anagalukira mfumu ya Asuri ndipo ankakana kuitumikira.+