2 Mafumu 18:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mʼchaka cha 4 cha Mfumu Hezekiya, chomwenso chinali chaka cha 7 cha Hoshiya+ mwana wa Ela mfumu ya Isiraeli, Salimanesere mfumu ya Asuri anapita kukaukira Samariya ndipo anazungulira mzindawo.+
9 Mʼchaka cha 4 cha Mfumu Hezekiya, chomwenso chinali chaka cha 7 cha Hoshiya+ mwana wa Ela mfumu ya Isiraeli, Salimanesere mfumu ya Asuri anapita kukaukira Samariya ndipo anazungulira mzindawo.+