2 Mafumu 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Asuriwo analanda mzindawo+ patatha zaka zitatu. Anaulanda mʼchaka cha 6 cha Hezekiya, chomwe chinali chaka cha 9 cha Hoshiya mfumu ya Isiraeli. Choncho Samariya analandidwa.
10 Asuriwo analanda mzindawo+ patatha zaka zitatu. Anaulanda mʼchaka cha 6 cha Hezekiya, chomwe chinali chaka cha 9 cha Hoshiya mfumu ya Isiraeli. Choncho Samariya analandidwa.