2 Mafumu 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako mfumu ya Asuri inatenga Aisiraeli nʼkupita nawo ku Asuri.+ Mfumuyo inakaika Aisiraeliwo ku Hala ndi ku Habori pafupi ndi mtsinje wa Gozani ndiponso mʼmizinda ya Amedi.+
11 Kenako mfumu ya Asuri inatenga Aisiraeli nʼkupita nawo ku Asuri.+ Mfumuyo inakaika Aisiraeliwo ku Hala ndi ku Habori pafupi ndi mtsinje wa Gozani ndiponso mʼmizinda ya Amedi.+