2 Mafumu 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mʼchaka cha 14 cha Mfumu Hezekiya, Senakeribu mfumu ya Asuri+ anabwera kudzaukira mizinda yonse ya Yuda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri ndipo analanda mizindayo.+ 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:13 Buku la Onse, ptsa. 14-15 Nsanja ya Olonda,6/1/1993, ptsa. 5-62/15/1988, ptsa. 27-28
13 Mʼchaka cha 14 cha Mfumu Hezekiya, Senakeribu mfumu ya Asuri+ anabwera kudzaukira mizinda yonse ya Yuda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri ndipo analanda mizindayo.+