2 Mafumu 18:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pa nthawi imeneyi Hezekiya mfumu ya Yuda anachotsa zitseko za kachisi+ wa Yehova ndi mafelemu ake, zimene iye anazikuta ndi golide,+ nʼkupereka golideyo kwa mfumu ya Asuri.
16 Pa nthawi imeneyi Hezekiya mfumu ya Yuda anachotsa zitseko za kachisi+ wa Yehova ndi mafelemu ake, zimene iye anazikuta ndi golide,+ nʼkupereka golideyo kwa mfumu ya Asuri.