2 Mafumu 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iwe wanena kuti, ‘Ndili ndi mphamvu komanso njira yabwino yomenyera nkhondoʼ koma mawu amenewa ndi osathandiza. Kodi ukudalira ndani pondigalukira ineyo?+
20 Iwe wanena kuti, ‘Ndili ndi mphamvu komanso njira yabwino yomenyera nkhondoʼ koma mawu amenewa ndi osathandiza. Kodi ukudalira ndani pondigalukira ineyo?+