2 Mafumu 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ukudalira thandizo la Iguputo,+ bango lophwanyika loti munthu ataligwira kuti alitsamire, lingamucheke mʼmanja. Ndi mmene zilili ndi Farao mfumu ya Iguputo kwa onse omudalira. 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:21 Nsanja ya Olonda,7/15/2010, ptsa. 12-138/1/2005, tsa. 11
21 Ukudalira thandizo la Iguputo,+ bango lophwanyika loti munthu ataligwira kuti alitsamire, lingamucheke mʼmanja. Ndi mmene zilili ndi Farao mfumu ya Iguputo kwa onse omudalira.