2 Mafumu 18:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ngati mungandiuze kuti, ‘Tikudalira Yehova Mulungu wathu,’+ kodi iyeyo si amene Hezekiya wamuchotsera malo ake okwezeka ndi maguwa ake ansembe+ nʼkuuza Yuda ndi Yerusalemu kuti, ‘Muzigwada patsogolo pa guwa lansembe la ku Yerusalemuliʼ?”’+ 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:22 Nsanja ya Olonda,7/15/2010, tsa. 13
22 Ngati mungandiuze kuti, ‘Tikudalira Yehova Mulungu wathu,’+ kodi iyeyo si amene Hezekiya wamuchotsera malo ake okwezeka ndi maguwa ake ansembe+ nʼkuuza Yuda ndi Yerusalemu kuti, ‘Muzigwada patsogolo pa guwa lansembe la ku Yerusalemuliʼ?”’+