-
2 Mafumu 18:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 mpaka ine nditabwera kudzakutengani nʼkupita nanu kudziko lofanana ndi lanulo,+ dziko la mbewu ndi la vinyo watsopano, dziko la mkate ndi minda ya mpesa, dziko la mitengo ya maolivi ndiponso la uchi. Mukatero mudzakhalabe ndi moyo. Musamumvere Hezekiya chifukwa akukunamizani pokuuzani kuti, ‘Yehova atipulumutsa.’
-