2 Mafumu 18:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Kodi milungu ya Hamati+ ndi Aripadi ili kuti? Nanga milungu ya Sefaravaimu,+ Hena ndi Iva ili kuti? Kodi yapulumutsa Samariya mʼmanja mwanga?+
34 Kodi milungu ya Hamati+ ndi Aripadi ili kuti? Nanga milungu ya Sefaravaimu,+ Hena ndi Iva ili kuti? Kodi yapulumutsa Samariya mʼmanja mwanga?+