-
2 Mafumu 18:37Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
37 Koma Eliyakimu mwana wa Hilikiya amene ankayangʼanira banja lachifumu, Sebina mlembi ndi Yowa mwana wa Asafu wolemba zochitika, anapita kwa Hezekiya atangʼamba zovala zawo ndipo anamuuza zomwe Rabisake ananena.
-