2 Mafumu 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako, inatuma Eliyakimu amene ankayangʼanira banja lachifumu, Sebina mlembi ndi akuluakulu a ansembe, onse atavala ziguduli, kuti apite kwa mneneri Yesaya+ mwana wa Amozi.
2 Kenako, inatuma Eliyakimu amene ankayangʼanira banja lachifumu, Sebina mlembi ndi akuluakulu a ansembe, onse atavala ziguduli, kuti apite kwa mneneri Yesaya+ mwana wa Amozi.