2 Mafumu 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo anamuuza kuti: “Hezekiya wanena kuti: ‘Lero ndi tsiku la zowawa, lonyozedwa ndi lochititsidwa manyazi. Chifukwa tili ngati akazi amene atsala pangʼono kubereka, koma alibe mphamvu zoti aberekere.+
3 Iwo anamuuza kuti: “Hezekiya wanena kuti: ‘Lero ndi tsiku la zowawa, lonyozedwa ndi lochititsidwa manyazi. Chifukwa tili ngati akazi amene atsala pangʼono kubereka, koma alibe mphamvu zoti aberekere.+