2 Mafumu 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Rabisake atamva kuti mfumu ya Asuri yachoka ku Lakisi+ anabwerera kwa mfumuyo ndipo anaipeza ikumenyana ndi Libina.+
8 Rabisake atamva kuti mfumu ya Asuri yachoka ku Lakisi+ anabwerera kwa mfumuyo ndipo anaipeza ikumenyana ndi Libina.+