2 Mafumu 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno Hezekiya anayamba kupemphera+ kwa Yehova kuti: “Inu Yehova Mulungu wa Isiraeli wokhala pamwamba* pa akerubi,+ inu nokha ndinu Mulungu woona wa maufumu onse apadziko lapansi.+ Inuyo munapanga kumwamba ndi dziko lapansi.
15 Ndiyeno Hezekiya anayamba kupemphera+ kwa Yehova kuti: “Inu Yehova Mulungu wa Isiraeli wokhala pamwamba* pa akerubi,+ inu nokha ndinu Mulungu woona wa maufumu onse apadziko lapansi.+ Inuyo munapanga kumwamba ndi dziko lapansi.