2 Mafumu 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Nʼzoonadi Yehova, kuti mafumu a Asuri awononga mayiko ndi anthu a mʼmayikowo.+