2 Mafumu 19:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kodi ndani amene iwe wamutonza ndi kumunyoza?+ Ndani amene iwe wamulankhula mokweza,+Ndiponso kumukwezera maso ako onyada? Ndi Woyera wa Isiraeli!+
22 Kodi ndani amene iwe wamutonza ndi kumunyoza?+ Ndani amene iwe wamulankhula mokweza,+Ndiponso kumukwezera maso ako onyada? Ndi Woyera wa Isiraeli!+