-
2 Mafumu 19:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Kudzera mwa anthu omwe unawatuma,+ wanyoza Yehova+ ndipo wanena kuti,
‘Ndi magaleta anga ankhondo ambiri,
Ndidzakwera pamwamba pa mapiri,
Ndidzafika kumadera akutali kwambiri a Lebanoni.
Ndidzadula mitengo yake ya mkungudza italiitali, ndi mitengo yake yabwino kwambiri ya junipa.*
Ndidzalowa kumalo ake akutali kwambiri, kunkhalango yowirira.
-