2 Mafumu 19:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Chifukwa kundipsera mtima kwako+ ndi kufuula kwako zafika mʼmakutu mwanga.+ Ndidzakola mphuno yako ndi ngowe yanga ndipo ndidzamanga zingwe zanga+ pakamwa pako.Kenako ndidzakukoka nʼkukubweza kudzera njira imene unadutsa pobwera.”+
28 Chifukwa kundipsera mtima kwako+ ndi kufuula kwako zafika mʼmakutu mwanga.+ Ndidzakola mphuno yako ndi ngowe yanga ndipo ndidzamanga zingwe zanga+ pakamwa pako.Kenako ndidzakukoka nʼkukubweza kudzera njira imene unadutsa pobwera.”+