2 Mafumu 19:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Chifukwa anthu otsala adzachokera ku Yerusalemu ndipo opulumuka adzachokera kuphiri la Ziyoni. Yehova wa magulu ankhondo akumwamba adzachita zimenezi modzipereka kwambiri.+
31 Chifukwa anthu otsala adzachokera ku Yerusalemu ndipo opulumuka adzachokera kuphiri la Ziyoni. Yehova wa magulu ankhondo akumwamba adzachita zimenezi modzipereka kwambiri.+