2 Mafumu 19:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Choncho Yehova wanena izi zokhudza mfumu ya Asuri:+ “Sadzalowa mumzindawu+Kapena kuponyamo muviKapena kufikamo ndi chishangoKapenanso kumanga malo okwera omenyerapo nkhondo atauzungulira.+ 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:32 Nsanja ya Olonda,2/15/1988, tsa. 28
32 Choncho Yehova wanena izi zokhudza mfumu ya Asuri:+ “Sadzalowa mumzindawu+Kapena kuponyamo muviKapena kufikamo ndi chishangoKapenanso kumanga malo okwera omenyerapo nkhondo atauzungulira.+