2 Mafumu 19:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Usiku umenewo, mngelo wa Yehova anapita kumsasa wa Asuri nʼkukapha asilikali 185,000.+ Anthu podzuka mʼmawa, anangoona kuti onse ndi mitembo yokhayokha.+ 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:35 Nsanja ya Olonda,6/1/1993, tsa. 62/15/1988, tsa. 28
35 Usiku umenewo, mngelo wa Yehova anapita kumsasa wa Asuri nʼkukapha asilikali 185,000.+ Anthu podzuka mʼmawa, anangoona kuti onse ndi mitembo yokhayokha.+