2 Mafumu 19:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Pamene Senakeribu ankaweramira mulungu wake Nisiroki mʼkachisi, ana ake Adarameleki ndi Sarezere anamupha ndi lupanga+ nʼkuthawira kudziko la Ararati.+ Kenako mwana wake Esari-hadoni+ anakhala mfumu mʼmalo mwake.
37 Pamene Senakeribu ankaweramira mulungu wake Nisiroki mʼkachisi, ana ake Adarameleki ndi Sarezere anamupha ndi lupanga+ nʼkuthawira kudziko la Ararati.+ Kenako mwana wake Esari-hadoni+ anakhala mfumu mʼmalo mwake.