2 Mafumu 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Yehova, chonde ndikukupemphani kuti mukumbukire kuti ndinayenda pamaso panu mokhulupirika ndiponso ndi mtima wonse komanso ndachita zabwino pamaso panu.”+ Kenako Hezekiya anayamba kulira kwambiri.
3 “Yehova, chonde ndikukupemphani kuti mukumbukire kuti ndinayenda pamaso panu mokhulupirika ndiponso ndi mtima wonse komanso ndachita zabwino pamaso panu.”+ Kenako Hezekiya anayamba kulira kwambiri.