2 Mafumu 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiwonjezera zaka 15 pa moyo* wako ndipo ndidzapulumutsa iweyo ndi mzindawu mʼmanja mwa mfumu ya Asuri.+ Ndidzateteza mzindawu chifukwa cha ineyo ndiponso chifukwa cha Davide mtumiki wanga.”’”+
6 Ndiwonjezera zaka 15 pa moyo* wako ndipo ndidzapulumutsa iweyo ndi mzindawu mʼmanja mwa mfumu ya Asuri.+ Ndidzateteza mzindawu chifukwa cha ineyo ndiponso chifukwa cha Davide mtumiki wanga.”’”+