2 Mafumu 20:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Hezekiya anali atafunsa Yesaya kuti: “Kodi chizindikiro+ chakuti Yehova andichiritsa ndipo ndidzapitadi kunyumba ya Yehova pa tsiku lachitatu nʼchiyani?”
8 Hezekiya anali atafunsa Yesaya kuti: “Kodi chizindikiro+ chakuti Yehova andichiritsa ndipo ndidzapitadi kunyumba ya Yehova pa tsiku lachitatu nʼchiyani?”