2 Mafumu 20:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yesaya anayankha kuti: “Chizindikiro chochokera kwa Yehova chosonyeza kuti Yehova adzakwaniritsadi mawu ake, ndi ichi: Kodi ukufuna kuti mthunzi uyende masitepe* 10 kupita kutsogolo, kapena uyende masitepe 10 kubwerera mʼmbuyo?”+
9 Yesaya anayankha kuti: “Chizindikiro chochokera kwa Yehova chosonyeza kuti Yehova adzakwaniritsadi mawu ake, ndi ichi: Kodi ukufuna kuti mthunzi uyende masitepe* 10 kupita kutsogolo, kapena uyende masitepe 10 kubwerera mʼmbuyo?”+