2 Mafumu 20:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho mneneri Yesaya anafuulira Yehova ndipo iye anachititsa mthunzi umene unali utapita kale kutsogolo kuti ubwerere mʼmbuyo pamasitepe a Ahazi. Mthunziwo unabwerera mʼmbuyo masitepe 10.+
11 Choncho mneneri Yesaya anafuulira Yehova ndipo iye anachititsa mthunzi umene unali utapita kale kutsogolo kuti ubwerere mʼmbuyo pamasitepe a Ahazi. Mthunziwo unabwerera mʼmbuyo masitepe 10.+