2 Mafumu 20:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa nthawi imeneyo, Berodaki-baladani mwana wa Baladani mfumu ya Babulo, anatumiza makalata ndi mphatso kwa Hezekiya chifukwa anamva kuti Hezekiya anadwala.+
12 Pa nthawi imeneyo, Berodaki-baladani mwana wa Baladani mfumu ya Babulo, anatumiza makalata ndi mphatso kwa Hezekiya chifukwa anamva kuti Hezekiya anadwala.+