-
2 Mafumu 20:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Hezekiya analandira anthuwo ndipo anawaonetsa nyumba yake yonse yosungiramo chuma.+ Anawaonetsa siliva, golide, mafuta a basamu, mafuta ena amtengo wapatali, nyumba yake yosungiramo zida zankhondo ndiponso chuma chake chonse. Palibe chimene Hezekiya sanawaonetse mʼnyumba yake* ndi mu ufumu wake wonse.
-