2 Mafumu 20:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 ‘Masiku akubwera pamene zinthu zonse zimene zili mʼnyumba mwako ndiponso zonse zimene makolo ako akhala akusunga mpaka lero, anthu adzazitenga nʼkupita nazo ku Babulo.+ Palibe chidzatsale,’ watero Yehova.
17 ‘Masiku akubwera pamene zinthu zonse zimene zili mʼnyumba mwako ndiponso zonse zimene makolo ako akhala akusunga mpaka lero, anthu adzazitenga nʼkupita nazo ku Babulo.+ Palibe chidzatsale,’ watero Yehova.