2 Mafumu 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anamanganso maguwa ansembe mʼnyumba ya Yehova,+ imene Yehova ananena kuti: “Ku Yerusalemu ndidzaikako dzina langa.”+
4 Anamanganso maguwa ansembe mʼnyumba ya Yehova,+ imene Yehova ananena kuti: “Ku Yerusalemu ndidzaikako dzina langa.”+