2 Mafumu 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye anamanga maguwa ansembe a gulu lonse la zinthu zakumwamba+ mʼmabwalo awiri a nyumba ya Yehova.+
5 Iye anamanga maguwa ansembe a gulu lonse la zinthu zakumwamba+ mʼmabwalo awiri a nyumba ya Yehova.+