2 Mafumu 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Manase anatentha* mwana wake wamwamuna pamoto, ankachita zamatsenga, ankawombeza+ ndiponso anaika anthu olankhula ndi mizimu komanso olosera zamʼtsogolo.+ Iye anachita zinthu zambiri zoipa pamaso pa Yehova ndiponso zomukwiyitsa.
6 Manase anatentha* mwana wake wamwamuna pamoto, ankachita zamatsenga, ankawombeza+ ndiponso anaika anthu olankhula ndi mizimu komanso olosera zamʼtsogolo.+ Iye anachita zinthu zambiri zoipa pamaso pa Yehova ndiponso zomukwiyitsa.