8 Sindidzachititsanso mapazi a Aisiraeli kuchoka mʼdziko limene ndinapatsa makolo awo,+ ngati atayesetsa kuchita zinthu mogwirizana ndi zonse zimene ndinawalamula,+ mogwirizana ndi Chilamulo chonse chimene Mose mtumiki wanga anawauza kuti azitsatira.”