2 Mafumu 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma sanamvere ndipo Manase anapitiriza kusocheretsa anthu ndiponso kuwachititsa zinthu zoipa kuposa zimene mitundu yomwe Yehova anaiwononga pamaso pa Aisiraeli inkachita.+
9 Koma sanamvere ndipo Manase anapitiriza kusocheretsa anthu ndiponso kuwachititsa zinthu zoipa kuposa zimene mitundu yomwe Yehova anaiwononga pamaso pa Aisiraeli inkachita.+