2 Mafumu 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Manase mfumu ya Yuda wachita zinthu zonyansa zonsezi. Wachita zinthu zoipa kwambiri kuposa zonse zimene anachita Aamori+ amene analiko iye asanakhale mfumu.+ Iye wachititsa Yuda kuchimwa ndi mafano ake onyansa.*
11 “Manase mfumu ya Yuda wachita zinthu zonyansa zonsezi. Wachita zinthu zoipa kwambiri kuposa zonse zimene anachita Aamori+ amene analiko iye asanakhale mfumu.+ Iye wachititsa Yuda kuchimwa ndi mafano ake onyansa.*