13 Ndidzayeza Yerusalemu ndi chingwe chimene ndinayezera+ Samariya+ ndiponso ndidzamuyeza ndi levulo imene ndinayezera nyumba ya Ahabu.+ Yerusalemu ndidzamʼpukuta mpaka kuyera ngati mmene munthu amapukutira mbale yolowa mpaka kuyera, nʼkuitembenuza.+