2 Mafumu 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako Manase, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo anaikidwa mʼmanda mʼmunda wapanyumba pake, mʼmunda wa Uziza.+ Ndiyeno mwana wake Amoni anakhala mfumu mʼmalo mwake.
18 Kenako Manase, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo anaikidwa mʼmanda mʼmunda wapanyumba pake, mʼmunda wa Uziza.+ Ndiyeno mwana wake Amoni anakhala mfumu mʼmalo mwake.