2 Mafumu 21:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma anthu a mʼdzikolo anapha anthu onse amene anakonzera chiwembu Mfumu Amoni. Kenako anthu amʼdzikolo anaika mwana wake Yosiya kuti akhale mfumu mʼmalo mwake.+
24 Koma anthu a mʼdzikolo anapha anthu onse amene anakonzera chiwembu Mfumu Amoni. Kenako anthu amʼdzikolo anaika mwana wake Yosiya kuti akhale mfumu mʼmalo mwake.+