2 Mafumu 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yosiya+ anayamba kulamulira ali ndi zaka 8 ndipo analamulira zaka 31 ku Yerusalemu.+ Mayi ake anali a ku Bozikati.+ Dzina lawo linali Yedida mwana wa Adaya.
22 Yosiya+ anayamba kulamulira ali ndi zaka 8 ndipo analamulira zaka 31 ku Yerusalemu.+ Mayi ake anali a ku Bozikati.+ Dzina lawo linali Yedida mwana wa Adaya.