2 Mafumu 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yosiya anachita zoyenera pamaso pa Yehova ndipo anayenda mʼnjira zonse za Davide kholo lake.+ Iye sanapatukire kumanja kapena kumanzere.
2 Yosiya anachita zoyenera pamaso pa Yehova ndipo anayenda mʼnjira zonse za Davide kholo lake.+ Iye sanapatukire kumanja kapena kumanzere.