2 Mafumu 22:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Pita kwa Hilikiya+ mkulu wa ansembe, ukamuuze kuti asonkhanitse ndalama zonse zimene zikubwera kunyumba ya Yehova,+ zimene alonda a pakhomo atolera kwa anthu.+
4 “Pita kwa Hilikiya+ mkulu wa ansembe, ukamuuze kuti asonkhanitse ndalama zonse zimene zikubwera kunyumba ya Yehova,+ zimene alonda a pakhomo atolera kwa anthu.+